Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Muzisamalira zonse zimene ndakuuzani,+ ndipo musatchule dzina la milungu ina. Lisamveke pakamwa panu.+

  • Deuteronomo 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+

  • Yesaya 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Milungu yopanda phindu idzatheratu.+

  • Ezekieli 36:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ine ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera. Ndidzakuyeretsani+ pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+

  • Zefaniya 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Ndidzatambasula dzanja langa ndi kuwononga Yuda pamodzi ndi anthu onse okhala mu Yerusalemu.+ Ndidzawononga anthu onse otsala amene amapembedza Baala+ ndi kuwachotsa pamalo ano. Ndidzafafanizanso dzina la ansembe a mulungu wachilendo pamodzi ndi ansembe ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena