Ezekieli 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Maguwa anu ansembe adzasiyidwa.+ Maguwa anu ofukizirapo zonunkhira adzaphwanyidwa, ndipo anthu anu ophedwa ndidzawagwetsera pamaso pa mafano anu onyansa.*+
4 Maguwa anu ansembe adzasiyidwa.+ Maguwa anu ofukizirapo zonunkhira adzaphwanyidwa, ndipo anthu anu ophedwa ndidzawagwetsera pamaso pa mafano anu onyansa.*+