Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndipo ndidzafafaniza malo anu opatulika olambirirako+ ndi kugwetsa maguwa anu ofukizirapo zonunkhira. Ndidzaponya mitembo yanu pamwamba pa mafano anu onyansa* opanda moyowo,+ ndipo mudzakhala onyansa kwa ine.+

  • 1 Mafumu 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno anafuulira guwa lansembelo mawu ochokera kwa Yehova oitanira tsoka, kuti: “Guwa lansembe iwe! Guwa lansembe iwe! Yehova wanena kuti, ‘Mwana wamwamuna adzabadwa m’nyumba ya Davide, dzina lake Yosiya.+ Ndithu adzatenga ansembe a malo okwezeka amene akufukiza nsembe yautsi pa iwe, n’kuwapereka nsembe pa iwe. Iye adzawotcha mafupa a anthu pa iwe.’”+

  • Yeremiya 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero ndisanawabwezeretse, ndidzawabwezera zolakwa zawo zonse+ ndi machimo awo onse chifukwa choipitsa dziko langa.+ Anadzaza cholowa changa ndi mitembo ya zinthu zawo zochititsa mseru ndiponso zinthu zawo zonyansazo.’”+

  • Ezekieli 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chotero ine ndinalowa, ndipo ndinaona kuti pamakoma anajambulapo zithunzi+ za nyama iliyonse yokwawa, za chilombo chilichonse chonyansa+ ndi za mafano onse onyansa a nyumba ya Isiraeli.+ Pamakoma onse anajambulapo zithunzizo mochita kugoba.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena