Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 11:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma pa zamoyo za m’madzi zopezeka zambiri ndi pa zamoyo zina zonse za m’madzi, chilichonse chimene chilibe zipsepse ndi mamba, chopezeka m’nyanja ndi m’mitsinje, chikhale chonyansa kwa inu.

  • Machitidwe 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pachinthu chimenecho panali mitundu yonse ya nyama za miyendo inayi, ndi zokwawa zapadziko lapansi, ndiponso mbalame zam’mlengalenga.+

  • Aroma 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 ndipo anasandutsa ulemerero+ wa Mulungu amene sawonongeka kukhala ngati chifaniziro+ cha munthu, mbalame, zolengedwa za miyendo inayi ndi zokwawa,+ zonsezo zimene zimawonongeka.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena