-
2 Mafumu 23:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Yosiya anachotsanso anthu olankhula ndi mizimu+ ndi olosera+ zam’tsogolo. Anachotsanso aterafi,*+ mafano onyansa,+ ndi zonyansa+ zonse zimene zinali m’dziko la Yuda ndi mu Yerusalemu, kuti atsatire mawu a chilamulo+ amene analembedwa m’buku+ limene wansembe Hilikiya analipeza panyumba ya Yehova.+
-