Levitiko 19:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “‘Musatembenukire kwa olankhula ndi mizimu+ ndipo musafunsire olosera zam’tsogolo+ ndi kudetsedwa nawo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Levitiko 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Mwamuna kapena mkazi amene amalankhula ndi mizimu kapena amene amalosera zam’tsogolo+ aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa mwa kuponyedwa miyala. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.’”+ 1 Samueli 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Samueli anali atamwalira ndipo Aisiraeli anali atamulira ndi kumuika m’manda mumzinda wakwawo ku Rama.+ Ndipo Sauli anali atachotsa anthu olankhula ndi mizimu ndi akatswiri olosera zam’tsogolo m’dzikolo.+
31 “‘Musatembenukire kwa olankhula ndi mizimu+ ndipo musafunsire olosera zam’tsogolo+ ndi kudetsedwa nawo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
27 “‘Mwamuna kapena mkazi amene amalankhula ndi mizimu kapena amene amalosera zam’tsogolo+ aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa mwa kuponyedwa miyala. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.’”+
3 Tsopano Samueli anali atamwalira ndipo Aisiraeli anali atamulira ndi kumuika m’manda mumzinda wakwawo ku Rama.+ Ndipo Sauli anali atachotsa anthu olankhula ndi mizimu ndi akatswiri olosera zam’tsogolo m’dzikolo.+