Deuteronomo 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 munaona zinthu zawo zonyansa ndi mafano awo onyansa,*+ mafano amtengo ndi amwala, asiliva ndi agolide amene anali nawo.) 1 Mafumu 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Solomo anayamba kutsatira Asitoreti,+ mulungu wamkazi wa Asidoni, ndi Milikomu,+ chonyansa cha Aamoni. 1 Mafumu 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anamangira Kemosi+ malo okwezeka,+ chinthu chonyansa+ cha Mowabu, paphiri+ lomwe linali patsogolo+ pa Yerusalemu. Anamangiranso Moleki malo okwezeka, yemwe ndi chinthu chonyansa cha ana a Amoni.
17 munaona zinthu zawo zonyansa ndi mafano awo onyansa,*+ mafano amtengo ndi amwala, asiliva ndi agolide amene anali nawo.)
5 Solomo anayamba kutsatira Asitoreti,+ mulungu wamkazi wa Asidoni, ndi Milikomu,+ chonyansa cha Aamoni.
7 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anamangira Kemosi+ malo okwezeka,+ chinthu chonyansa+ cha Mowabu, paphiri+ lomwe linali patsogolo+ pa Yerusalemu. Anamangiranso Moleki malo okwezeka, yemwe ndi chinthu chonyansa cha ana a Amoni.