Numeri 33:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+ Deuteronomo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mudzawononge+ malo onse amene ali pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mitengo ikuluikulu ya masamba obiriwira, pamene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo.+
52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+
2 Mudzawononge+ malo onse amene ali pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mitengo ikuluikulu ya masamba obiriwira, pamene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo.+