-
2 Mafumu 23:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Yosiya atatembenuka, anaona manda amene anali m’phirimo. Choncho anatumiza anthu kuti akatenge mafupa m’mandawo, ndipo anawatentha+ paguwa lansembelo kuti alisandutse losayenera kulambirapo, mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene munthu wa Mulungu woona uja, amene analengeza+ zinthu zimenezi, ananena.
-