Ekisodo 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwatambasula dzanja lanu lamanja,+ ndipo dziko lawameza.+ Yesaya 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti Yehova wa makamu wagamula,+ ndani angazilepheretse?+ Dzanja lake n’limene latambasuka, ndani angalibweze?+ Yeremiya 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ‘Pakuti ana a Yuda achita zinthu zoipa m’maso mwanga,’ watero Yehova. ‘Aika zinthu zawo zonyansa m’nyumba yotchedwa ndi dzina langa kuti aiipitse.+
27 Pakuti Yehova wa makamu wagamula,+ ndani angazilepheretse?+ Dzanja lake n’limene latambasuka, ndani angalibweze?+
30 ‘Pakuti ana a Yuda achita zinthu zoipa m’maso mwanga,’ watero Yehova. ‘Aika zinthu zawo zonyansa m’nyumba yotchedwa ndi dzina langa kuti aiipitse.+