Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 40:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Kodi ndithu ukuchititsa chilungamo changa kukhala chopanda pake?

      Kodi ukunena kuti ine ndine wolakwa kuti iweyo ukhale wolondola?+

  • Salimo 33:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Zolinga za Yehova zidzakhalapo mpaka kalekale.+

      Maganizo a mumtima mwake adzakhalapo ku mibadwomibadwo.+

  • Miyambo 19:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mumtima mwa munthu mumakhala zolinga zambiri,+ koma zolinga za Yehova n’zimene zidzakwaniritsidwe.+

  • Yesaya 46:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ine ndi amene ndidzaitane mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa.+ Ndidzaitana munthu kuti adzachite zolingalira zanga kuchokera kutali.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita.+ Ndakonza zimenezi ndipo ndidzazichitadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena