Salimo 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+ Aroma 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ayi! Koma Mulungu akhale wonena zoona,+ ngakhale kuti munthu aliyense angapezeke kukhala wonama,+ monganso Malemba amanenera kuti: “Mukamalankhula mumalankhula zachilungamo, kuti mupambane pamene mukuweruzidwa.”+
4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+
4 Ayi! Koma Mulungu akhale wonena zoona,+ ngakhale kuti munthu aliyense angapezeke kukhala wonama,+ monganso Malemba amanenera kuti: “Mukamalankhula mumalankhula zachilungamo, kuti mupambane pamene mukuweruzidwa.”+