Salimo 116:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene ndinapanikizika ndinati:+“Munthu aliyense ndi wabodza.”+ Yeremiya 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu anzeru achita manyazi.+ Achita mantha ndipo adzagwidwa. Taonani! Iwo akana mawu a Yehova. Kodi ali ndi nzeru yotani tsopano?+ Yeremiya 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense amapusitsa mnzake+ ndipo salankhula choonadi ngakhale pang’ono. Aphunzitsa lilime lawo kulankhula chinyengo.+ Iwo adzitopetsa okha ndi kuchita zinthu zoipa.+
9 Anthu anzeru achita manyazi.+ Achita mantha ndipo adzagwidwa. Taonani! Iwo akana mawu a Yehova. Kodi ali ndi nzeru yotani tsopano?+
5 Aliyense amapusitsa mnzake+ ndipo salankhula choonadi ngakhale pang’ono. Aphunzitsa lilime lawo kulankhula chinyengo.+ Iwo adzitopetsa okha ndi kuchita zinthu zoipa.+