Genesis 31:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma bambo anu akhala akundipusitsa, ndipo asintha malipiro anga maulendo 10. Ngakhale ndi choncho, Mulungu sanawalole kuti andichite choipa.+ Yobu 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi zolankhula zako zopanda pake zingachititse anthu kukhala chete?Ndipo kodi upitirizabe kunyoza popanda wokudzudzula?+
7 Koma bambo anu akhala akundipusitsa, ndipo asintha malipiro anga maulendo 10. Ngakhale ndi choncho, Mulungu sanawalole kuti andichite choipa.+
3 Kodi zolankhula zako zopanda pake zingachititse anthu kukhala chete?Ndipo kodi upitirizabe kunyoza popanda wokudzudzula?+