Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+

      Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+

      ע [ʽAʹyin]

      Adzawateteza mpaka kalekale.+

      Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+

  • Mlaliki 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ngakhale woipa atachita zoipa+ maulendo 100 n’kukhala ndi moyo wautali akuchitabe zofuna zake, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino,+ chifukwa chakuti anali kumuopa.+

  • Yesaya 54:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chida chilichonse chimene chidzapangidwe kuti chikuvulaze sichidzapambana,+ ndipo lilime lililonse limene lidzalimbane nawe pamlandu udzalitsutsa.+ Ichi ndi cholowa cha atumiki a Yehova,+ ndipo chilungamo chawo n’chochokera kwa ine,” akutero Yehova.+

  • 1 Petulo 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndithudi, ndani angakuchitireni zoipa mukakhala odzipereka pochita zabwino?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena