1 Mafumu 18:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anthu onsewo ataona zimenezo, nthawi yomweyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo ananena kuti: “Yehova ndiye Mulungu woona! Yehova ndiye Mulungu woona!” Yohane 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amene walandira umboni wakewo waika chisindikizo chake pa umboniwo chakuti Mulungu amanena zoona.+ Yohane 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndili ndi zambiri zoti ndinene zokhudza inu ndi kuperekerapo chiweruzo. Ndipotu amene anandituma ine amanena zoona. Zimene ndinamva kwa iye, zomwezo ndikuzilankhula m’dzikoli.”+
39 Anthu onsewo ataona zimenezo, nthawi yomweyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo ananena kuti: “Yehova ndiye Mulungu woona! Yehova ndiye Mulungu woona!”
33 Amene walandira umboni wakewo waika chisindikizo chake pa umboniwo chakuti Mulungu amanena zoona.+
26 Ndili ndi zambiri zoti ndinene zokhudza inu ndi kuperekerapo chiweruzo. Ndipotu amene anandituma ine amanena zoona. Zimene ndinamva kwa iye, zomwezo ndikuzilankhula m’dzikoli.”+