Aroma 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ayi! Koma Mulungu akhale wonena zoona,+ ngakhale kuti munthu aliyense angapezeke kukhala wonama,+ monganso Malemba amanenera kuti: “Mukamalankhula mumalankhula zachilungamo, kuti mupambane pamene mukuweruzidwa.”+ 1 Yohane 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wokhulupirira Mwana wa Mulungu ndiye kuti walandira umboni+ umene wapatsidwa. Munthu wosakhulupirira Mulungu ndiye kuti akumuona ngati wonama,+ chifukwa sanakhulupirire kuti zimene Mulungu wanena+ zokhudza Mwana wake, ndi zoona.+
4 Ayi! Koma Mulungu akhale wonena zoona,+ ngakhale kuti munthu aliyense angapezeke kukhala wonama,+ monganso Malemba amanenera kuti: “Mukamalankhula mumalankhula zachilungamo, kuti mupambane pamene mukuweruzidwa.”+
10 Munthu wokhulupirira Mwana wa Mulungu ndiye kuti walandira umboni+ umene wapatsidwa. Munthu wosakhulupirira Mulungu ndiye kuti akumuona ngati wonama,+ chifukwa sanakhulupirire kuti zimene Mulungu wanena+ zokhudza Mwana wake, ndi zoona.+