-
Yesaya 41:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Kodi ndani anautsa winawake kuchokera kotulukira dzuwa?+ Kodi ndani anamuitana mwachilungamo kuti ayandikire kumapazi ake, kuti amupatse mitundu ya anthu pamaso pake, ndiponso kuti amuchititse kupita kukagonjetsa ngakhale mafumu?+ Kodi ndani amene anali kuwapereka kulupanga lake ngati fumbi, moti auluzika ndi uta wake ngati mapesi?+
-