Yesaya 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire.+ Iwowa amaona kuti siliva si kanthu, ndipo sasangalala ndi golide. Yesaya 41:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ine ndautsa winawake kuchokera kumpoto, ndipo abwera.+ Iye adzaitana pa dzina langa kuchokera kotulukira dzuwa.+ Adzaukira atsogoleri ngati kuti ndi dongo+ ndiponso ngati kuti iyeyo ndi woumba amene amapondaponda dongo laliwisi. Yeremiya 51:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Iwe ndiwe chibonga changa, zida zanga zankhondo.+ Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya mitundu ya anthu kukhala zidutswazidutswa. Kudzera mwa iwe ndidzawononga maufumu.
17 “Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire.+ Iwowa amaona kuti siliva si kanthu, ndipo sasangalala ndi golide.
25 “Ine ndautsa winawake kuchokera kumpoto, ndipo abwera.+ Iye adzaitana pa dzina langa kuchokera kotulukira dzuwa.+ Adzaukira atsogoleri ngati kuti ndi dongo+ ndiponso ngati kuti iyeyo ndi woumba amene amapondaponda dongo laliwisi.
20 “Iwe ndiwe chibonga changa, zida zanga zankhondo.+ Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya mitundu ya anthu kukhala zidutswazidutswa. Kudzera mwa iwe ndidzawononga maufumu.