Yesaya 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndi amene ndidzaitane mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa.+ Ndidzaitana munthu kuti adzachite zolingalira zanga kuchokera kutali.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita.+ Ndakonza zimenezi ndipo ndidzazichitadi.+ Chivumbulutso 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mngelo wa 6+ anathira mbale yake pamtsinje waukulu wa Firate,+ ndipo madzi ake anauma,+ kuti njira ya mafumu+ ochokera kotulukira dzuwa ikonzedwe.
11 Ine ndi amene ndidzaitane mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa.+ Ndidzaitana munthu kuti adzachite zolingalira zanga kuchokera kutali.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita.+ Ndakonza zimenezi ndipo ndidzazichitadi.+
12 Mngelo wa 6+ anathira mbale yake pamtsinje waukulu wa Firate,+ ndipo madzi ake anauma,+ kuti njira ya mafumu+ ochokera kotulukira dzuwa ikonzedwe.