Yobu 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye ali ndi maganizo amodzi, ndani angam’tsutse?+Zimene moyo wake umalakalaka amazichita.+