Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pamenepo Yehova anati: “Taonani! Izi n’zimene anthuwa ayamba kuchita popeza ndi amodzi ndipo onse ali ndi chilankhulo chimodzi.+ Mmene zililimu, angathe kuchita chilichonse chimene akuganiza.+

  • Esitere 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma Esitere ataonekera pamaso pa mfumu, mfumuyo inalemba lamulo lakuti:+ “Chiwembu+ chake choipa chimene anakonzera Ayuda chimugwere iyeyo.”+ Choncho Hamani komanso ana ake anawapachika pamtengo.+

  • Salimo 21:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti akuchitirani zinthu zoipa.+

      Alinganiza kuchita zinthu zimene sangazikwanitse.+

  • Miyambo 16:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Munthu angaganize za njira zake mumtima mwake,+ koma Yehova ndiye amawongolera mayendedwe ake.+

  • Mlaliki 7:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Zimene ndapeza n’zakuti, Mulungu woona anapanga anthu owongoka mtima,+ koma anthuwo asankha njira zina zambirimbiri.”+

  • Chivumbulutso 17:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mafumuwa maganizo awo ndi amodzi, choncho adzapereka mphamvu zawo ndi ulamuliro wawo kwa chilombocho.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena