Salimo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe,+Ndiponso n’chifukwa chiyani mitundu ya anthu ikung’ung’udza za chinthu chopanda pake?+ Salimo 83:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anena kuti: “Bwerani tiwafafanize kuti asakhalenso mtundu,+Ndi kuti dzina la Isiraeli lisakumbukikenso.”+
2 N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe,+Ndiponso n’chifukwa chiyani mitundu ya anthu ikung’ung’udza za chinthu chopanda pake?+
4 Iwo anena kuti: “Bwerani tiwafafanize kuti asakhalenso mtundu,+Ndi kuti dzina la Isiraeli lisakumbukikenso.”+