Ekisodo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tiyeni tiwachenjerere,+ kuti asapitirize kuchulukana kuopera kuti pa nthawi ya nkhondo angadzagwirizane ndi adani athu ndi kumenyana nafe n’kuchoka m’dziko lino.” 2 Mbiri 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pake ana a Mowabu,+ ana a Amoni,+ pamodzi ndi Aamonimu+ ena, anabwera kudzamenyana ndi Yehosafati.+ Esitere 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Hamani anaona kuti n’zosakwanira kupha Moredekai yekha pakuti anthu anamuuza za anthu a mtundu wa Moredekai. Choncho Hamani anayamba kufunafuna kufafaniza+ Ayuda onse, anthu a mtundu wa Moredekai amene anali mu ufumu wonse wa Ahasiwero.+
10 Tiyeni tiwachenjerere,+ kuti asapitirize kuchulukana kuopera kuti pa nthawi ya nkhondo angadzagwirizane ndi adani athu ndi kumenyana nafe n’kuchoka m’dziko lino.”
20 Pambuyo pake ana a Mowabu,+ ana a Amoni,+ pamodzi ndi Aamonimu+ ena, anabwera kudzamenyana ndi Yehosafati.+
6 Koma Hamani anaona kuti n’zosakwanira kupha Moredekai yekha pakuti anthu anamuuza za anthu a mtundu wa Moredekai. Choncho Hamani anayamba kufunafuna kufafaniza+ Ayuda onse, anthu a mtundu wa Moredekai amene anali mu ufumu wonse wa Ahasiwero.+