Salimo 105:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Analola adaniwo kusintha mitima yawo ndi kudana ndi anthu ake,+Anawalola kuchitira atumiki ake zachinyengo.+ Miyambo 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira kulikonse, kapena malangizo alionse otsutsana ndi Yehova.+ Machitidwe 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mfumu imeneyi inagwiritsa ntchito ulamuliro wake molakwika pofuna kuzunza anthu a fuko lathu,+ ndipo mwankhanza inachititsa makolo athuwo kutaya makanda awo, kuti asakhale ndi moyo.+ 1 Akorinto 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti kwa Mulungu nzeru za m’dzikoli n’zopusa,+ chifukwa Malemba amati: “Iye amakola anzeru m’kuchenjera kwawo.”+
25 Analola adaniwo kusintha mitima yawo ndi kudana ndi anthu ake,+Anawalola kuchitira atumiki ake zachinyengo.+
19 Mfumu imeneyi inagwiritsa ntchito ulamuliro wake molakwika pofuna kuzunza anthu a fuko lathu,+ ndipo mwankhanza inachititsa makolo athuwo kutaya makanda awo, kuti asakhale ndi moyo.+
19 Pakuti kwa Mulungu nzeru za m’dzikoli n’zopusa,+ chifukwa Malemba amati: “Iye amakola anzeru m’kuchenjera kwawo.”+