Ekisodo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tiyeni tiwachenjerere,+ kuti asapitirize kuchulukana kuopera kuti pa nthawi ya nkhondo angadzagwirizane ndi adani athu ndi kumenyana nafe n’kuchoka m’dziko lino.”
10 Tiyeni tiwachenjerere,+ kuti asapitirize kuchulukana kuopera kuti pa nthawi ya nkhondo angadzagwirizane ndi adani athu ndi kumenyana nafe n’kuchoka m’dziko lino.”