Ekisodo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Farao analamula anthu ake onse kuti: “Mwana aliyense wamwamuna wa Aheberi wobadwa kumene, muzim’ponya mumtsinje wa Nailo, koma mwana aliyense wamkazi muzimusiya wamoyo.”+
22 Kenako Farao analamula anthu ake onse kuti: “Mwana aliyense wamwamuna wa Aheberi wobadwa kumene, muzim’ponya mumtsinje wa Nailo, koma mwana aliyense wamkazi muzimusiya wamoyo.”+