2 Mbiri 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano taonani zimene akuchita ana a Amoni,+ ana a Mowabu+ ndi a kudera lamapiri la Seiri.+ Inu simunalole kuti Aisiraeli alowe m’dziko lawo pamene anali kutuluka m’dziko la Iguputo ndipo anawasiya osawawononga.+
10 Tsopano taonani zimene akuchita ana a Amoni,+ ana a Mowabu+ ndi a kudera lamapiri la Seiri.+ Inu simunalole kuti Aisiraeli alowe m’dziko lawo pamene anali kutuluka m’dziko la Iguputo ndipo anawasiya osawawononga.+