Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chonde mutilole tidzere m’dziko lanu. Sitidzera m’munda wanu uliwonse, kapena m’munda wa mpesa uliwonse. Sitimwa madzi a pachitsime chanu chilichonse. Tizingoyenda+ mumsewu wa mfumu, osapatukira kudzanja lamanja kapena lamanzere,+ mpaka titadutsa m’dziko lanu.’”

  • Numeri 20:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Choncho mfumu ya Edomu inakana kulola Aisiraeli kudzera m’dziko lake.+ Motero, Aisiraeli analambalala dziko la Edomu.+

  • Deuteronomo 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Musalimbane nawo, chifukwa sindikupatsani dziko lawo, ngakhale kachigawo kokwana phazi limodzi lokha. Ndinapereka phiri la Seiri kwa Esau kuti likhale malo ake.+

  • Deuteronomo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo Yehova anandiuza kuti, ‘Usavutitse Amowabu kapena kuchita nawo nkhondo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko lawo kuti likhale lako. Ndinapereka Ari+ kwa ana a Loti kuti akhale malo awo.+

  • Deuteronomo 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 ndipo uyandikire pafupi ndi ana a Amoni. Usawavutitse kapena kumenyana nawo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko la ana a Amoni kuti likhale lako. Dziko limeneli ndinalipereka kwa ana a Loti kuti likhale lawo.+

  • Oweruza 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 ndipo anaiuza kuti:

      “Yefita wanena kuti, ‘Aisiraeli sanatenge dziko la Mowabu+ ndi dziko la ana a Amoni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena