Numeri 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mitsinje ya m’zigwazo imakafika ku Ari+ ndipo imayenda m’malire a dziko la Mowabu.” Deuteronomo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ‘Lero udutsa m’dera la Mowabu, pafupi ndi Ari,+ Yesaya 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uwu ndi uthenga wokhudza Mowabu:+ Chifukwa chakuti wasakazidwa usiku, Ari+ wa ku Mowabu wakhala chete. Chifukwa chakuti wasakazidwa usiku, Kiri+ wa ku Mowabu wakhala chete.
15 Uwu ndi uthenga wokhudza Mowabu:+ Chifukwa chakuti wasakazidwa usiku, Ari+ wa ku Mowabu wakhala chete. Chifukwa chakuti wasakazidwa usiku, Kiri+ wa ku Mowabu wakhala chete.