Numeri 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mitsinje ya m’zigwazo imakafika ku Ari+ ndipo imayenda m’malire a dziko la Mowabu.” Numeri 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti moto watuluka ku Hesiboni,+ lawi lamoto latuluka m’tauni ya Sihoni.Lanyeketsa Ari+ mzinda wa ku Mowabu, lanyeketsa eni ake a malo okwezeka a ku Arinoni.
28 Pakuti moto watuluka ku Hesiboni,+ lawi lamoto latuluka m’tauni ya Sihoni.Lanyeketsa Ari+ mzinda wa ku Mowabu, lanyeketsa eni ake a malo okwezeka a ku Arinoni.