Yeremiya 48:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 ‘Anthu othawa aima chilili mumthunzi wa Hesiboni ndipo alibe mphamvu. Moto udzachokera ku Hesiboni+ ndipo malawi a moto adzachokera ku Sihoni+ ndi kutentha Mowabu m’mutu, m’mphepete mwa makutu, komanso paliwombo pa ana osokoneza.’+
45 ‘Anthu othawa aima chilili mumthunzi wa Hesiboni ndipo alibe mphamvu. Moto udzachokera ku Hesiboni+ ndipo malawi a moto adzachokera ku Sihoni+ ndi kutentha Mowabu m’mutu, m’mphepete mwa makutu, komanso paliwombo pa ana osokoneza.’+