Yeremiya 48:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 ‘Anthu amene akuthawa aima mumthunzi wa Hesiboni ndipo alibe mphamvu. Chifukwa moto udzachokera ku HesiboniNdipo malawi a moto adzachokera ku Sihoni.+ Motowo udzawotcha Mowabu pachipumiKomanso mitu ya ana achiwawa.+
45 ‘Anthu amene akuthawa aima mumthunzi wa Hesiboni ndipo alibe mphamvu. Chifukwa moto udzachokera ku HesiboniNdipo malawi a moto adzachokera ku Sihoni.+ Motowo udzawotcha Mowabu pachipumiKomanso mitu ya ana achiwawa.+