-
Yoswa 13:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 mizinda yonse ya m’malo okwererapo,+ ndiponso dziko lonse la Sihoni mfumu ya Aamori imene inali kulamulira ili ku Hesiboni.+ Mfumu imeneyi Mose anaipha+ limodzi ndi atsogoleri a ku Midiyani, Evi, Rekemu, Zuri, Hura, ndi Reba.+ Amenewa anali mafumu omwe anali pansi pa Sihoni ndipo anali kukhala m’dzikolo.
-