Oweruza 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Kenako Aisiraeli anatumiza mithenga kwa Sihoni mfumu ya Aamori, ya ku Hesiboni,+ kuti: “Tiloleni tidutse m’dziko lanu kupita kumalo athu.”+
19 “‘Kenako Aisiraeli anatumiza mithenga kwa Sihoni mfumu ya Aamori, ya ku Hesiboni,+ kuti: “Tiloleni tidutse m’dziko lanu kupita kumalo athu.”+