Numeri 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mitsinje ya m’zigwazo imakafika ku Ari+ ndipo imayenda m’malire a dziko la Mowabu.” Deuteronomo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yehova anandiuza kuti, ‘Usavutitse Amowabu kapena kuchita nawo nkhondo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko lawo kuti likhale lako. Ndinapereka Ari+ kwa ana a Loti kuti akhale malo awo.+
9 Pamenepo Yehova anandiuza kuti, ‘Usavutitse Amowabu kapena kuchita nawo nkhondo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko lawo kuti likhale lako. Ndinapereka Ari+ kwa ana a Loti kuti akhale malo awo.+