29 monga mmene ana a Esau amene akukhala m’Seiri+ ndi Amowabu+ amene akukhala mu Ari anachitira kwa ine. Ndidzadutsa m’dziko lako mpaka kukawoloka Yorodano, kulowa m’dziko limene Yehova Mulungu wathu anatipatsa.’+
15Uwu ndi uthenga wokhudza Mowabu:+ Chifukwa chakuti wasakazidwa usiku, Ari+ wa ku Mowabu wakhala chete. Chifukwa chakuti wasakazidwa usiku, Kiri+ wa ku Mowabu wakhala chete.