Deuteronomo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yehova anandiuza kuti, ‘Usavutitse Amowabu kapena kuchita nawo nkhondo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko lawo kuti likhale lako. Ndinapereka Ari+ kwa ana a Loti kuti akhale malo awo.+ Deuteronomo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ‘Lero udutsa m’dera la Mowabu, pafupi ndi Ari,+
9 Pamenepo Yehova anandiuza kuti, ‘Usavutitse Amowabu kapena kuchita nawo nkhondo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko lawo kuti likhale lako. Ndinapereka Ari+ kwa ana a Loti kuti akhale malo awo.+