Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 3:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno Aisiraeliwo anayamba kugwetsa mizinda.+ Pamalo alionse abwino, aliyense anali kuponyapo mwala mpaka kudzaza malo onsewo. Anatseka kasupe aliyense wamadzi+ ndi kugwetsa mtengo uliwonse wabwino.+ Koma miyala ya mzinda wa Kiri-hareseti+ yokha anaisiya. Oponya miyala anazungulira mzindawo n’kuuponya miyala.

  • Yeremiya 48:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 N’chifukwa chake Mowabu ndidzamukuwira, ndipo ndidzafuulira Mowabu yense.+ Anthu adzalirira amuna a ku Kiri-haresi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena