Genesis 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zitsime zonse zimene antchito a Abulahamu bambo ake anakumba m’masiku a bambo akewo,+ Afilisiti anazifotsera ndi dothi.+ 2 Mbiri 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero anthu ambiri anasonkhana ndipo anapita kukatseka akasupe onse ndi mtsinje+ umene unkasefukira kudutsa pakati pa dzikolo, popeza anati: “Sitikufuna kuti mafumu a Asuri akabwera adzapeze madzi ochuluka.”
15 Zitsime zonse zimene antchito a Abulahamu bambo ake anakumba m’masiku a bambo akewo,+ Afilisiti anazifotsera ndi dothi.+
4 Chotero anthu ambiri anasonkhana ndipo anapita kukatseka akasupe onse ndi mtsinje+ umene unkasefukira kudutsa pakati pa dzikolo, popeza anati: “Sitikufuna kuti mafumu a Asuri akabwera adzapeze madzi ochuluka.”