2 Mbiri 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako iwo ananyamuka n’kuchotsa maguwa ansembe+ amene anali mu Yerusalemu. Anachotsanso maguwa ansembe onse ofukizirapo+ n’kukawataya kuchigwa cha Kidironi.+
14 Kenako iwo ananyamuka n’kuchotsa maguwa ansembe+ amene anali mu Yerusalemu. Anachotsanso maguwa ansembe onse ofukizirapo+ n’kukawataya kuchigwa cha Kidironi.+