2 Samueli 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Anthu onse a m’dzikoli anali kulira mokweza mawu,+ ndipo anthu onse amene anali ndi Davide anali kudutsa pamaso pake. Mfumu inaimirira pafupi ndi chigwa* cha Kidironi,+ ndipo anthu onse anali kudutsa mumsewu waukulu wopita kuchipululu.
23 Anthu onse a m’dzikoli anali kulira mokweza mawu,+ ndipo anthu onse amene anali ndi Davide anali kudutsa pamaso pake. Mfumu inaimirira pafupi ndi chigwa* cha Kidironi,+ ndipo anthu onse anali kudutsa mumsewu waukulu wopita kuchipululu.