1 Mafumu 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Zikadzachitika kuti tsiku lina wachoka n’kudutsa chigwa* cha Kidironi,+ udziwiretu kuti udzafa ndithu.+ Mlandu wa magazi ako udzakhala pamutu pako.”+ 2 Mbiri 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako iwo ananyamuka n’kuchotsa maguwa ansembe+ amene anali mu Yerusalemu. Anachotsanso maguwa ansembe onse ofukizirapo+ n’kukawataya kuchigwa cha Kidironi.+ Yohane 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atanena zimenezi, Yesu anatuluka pamodzi ndi ophunzira ake ndi kuwoloka khwawa la Kidironi,+ kupita kumene kunali munda. Ndipo iye ndi ophunzira akewo analowa m’mundamo.+
37 Zikadzachitika kuti tsiku lina wachoka n’kudutsa chigwa* cha Kidironi,+ udziwiretu kuti udzafa ndithu.+ Mlandu wa magazi ako udzakhala pamutu pako.”+
14 Kenako iwo ananyamuka n’kuchotsa maguwa ansembe+ amene anali mu Yerusalemu. Anachotsanso maguwa ansembe onse ofukizirapo+ n’kukawataya kuchigwa cha Kidironi.+
18 Atanena zimenezi, Yesu anatuluka pamodzi ndi ophunzira ake ndi kuwoloka khwawa la Kidironi,+ kupita kumene kunali munda. Ndipo iye ndi ophunzira akewo analowa m’mundamo.+