Mateyu 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako Yesu anafika nawo pamalo+ otchedwa Getsemane, ndipo anauza ophunzirawo kuti: “Khalani pansi pompano, ine ndikupita uko kukapemphera.”+ Maliko 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako anafika pamalo otchedwa Getsemane, ndipo anauza ophunzira akewo kuti: “Khalani pansi pompano, ine ndikukapemphera.”+
36 Kenako Yesu anafika nawo pamalo+ otchedwa Getsemane, ndipo anauza ophunzirawo kuti: “Khalani pansi pompano, ine ndikupita uko kukapemphera.”+
32 Kenako anafika pamalo otchedwa Getsemane, ndipo anauza ophunzira akewo kuti: “Khalani pansi pompano, ine ndikukapemphera.”+