Numeri 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 wobwezera magazi+ n’kumupeza kunja kwa malire a mzinda wothawirako, n’kumupha, wobwezera magaziyo alibe mlandu wa magazi. Miyambo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mfumu imakhala pampando wachiweruzo+ n’kubalalitsa zoipa zonse ndi maso ake.+ Miyambo 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mfumu yanzeru imabalalitsa anthu oipa,+ ndipo imawaponda ndi wilo lopunthira.+
27 wobwezera magazi+ n’kumupeza kunja kwa malire a mzinda wothawirako, n’kumupha, wobwezera magaziyo alibe mlandu wa magazi.