2 Samueli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 pamene munthu wina anandibweretsera uthenga+ wakuti, ‘Sauli wafa,’ ndipo iye anali kuganiza kuti wabweretsa uthenga wabwino, ine ndinamugwira ndi kumupha+ ku Zikilaga m’malo momulipira monga mthenga. Salimo 101:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’mawa uliwonse ndidzawononga oipa onse a padziko lapansi.+Ndidzapha ndi kuchotsa mumzinda wa Yehova anthu onse ochita zinthu zopweteka anzawo.+ Miyambo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mfumu imakhala pampando wachiweruzo+ n’kubalalitsa zoipa zonse ndi maso ake.+
10 pamene munthu wina anandibweretsera uthenga+ wakuti, ‘Sauli wafa,’ ndipo iye anali kuganiza kuti wabweretsa uthenga wabwino, ine ndinamugwira ndi kumupha+ ku Zikilaga m’malo momulipira monga mthenga.
8 M’mawa uliwonse ndidzawononga oipa onse a padziko lapansi.+Ndidzapha ndi kuchotsa mumzinda wa Yehova anthu onse ochita zinthu zopweteka anzawo.+