1 Mafumu 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Aisiraeli onse anamva za chigamulo+ chimene mfumu inapereka, ndipo anachita mantha chifukwa cha mfumuyo,+ popeza anaona kuti nzeru+ za Mulungu zinali mwa iye kuti azipereka zigamulo. Salimo 72:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aweruze osautsika pakati pa anthu,+Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo. Miyambo 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuchita zinthu zoipa kumanyansa mafumu,+ chifukwa mpando wachifumu umakhazikika ndi chilungamo.+
28 Aisiraeli onse anamva za chigamulo+ chimene mfumu inapereka, ndipo anachita mantha chifukwa cha mfumuyo,+ popeza anaona kuti nzeru+ za Mulungu zinali mwa iye kuti azipereka zigamulo.
4 Aweruze osautsika pakati pa anthu,+Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo.