Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 7:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Iweyo Ezara, pogwiritsa ntchito nzeru+ zimene Mulungu wako wakupatsa, uike anthu osungitsa malamulo ndi oweruza kuti nthawi zonse aziweruza+ anthu onse a kutsidya lina la Mtsinje, ngakhalenso onse odziwa malamulo a Mulungu wako. Aliyense wosadziwa malamulowo, amuna inu mum’phunzitse.+

  • Miyambo 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 komanso ukaitana kumvetsa zinthu+ ndi kufuulira kuzindikira,+

  • Mlaliki 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nzeru zimapangitsa munthu kukhala wamphamvu kuposa atsogoleri 10 amphamvu amene ali mumzinda.+

  • Akolose 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chuma chonse chokhudzana ndi nzeru ndiponso kudziwa zinthu+ chinabisidwa mosamala mwa iye.

  • Yakobo 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena