2 Samueli 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno mkazi wina wanzeru+ mumzindawo anayamba kufuula kuti: “Tamverani amuna inu, tamverani! Chonde muuzeni Yowabu kuti abwere pafupipa kuti ndilankhule naye.” Miyambo 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Wanzeru amakwera mzinda wa anthu amphamvu, kuti athetse mphamvu imene mzindawo umadalira.+ Miyambo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu amene amagwiritsa ntchito mphamvu zake mwanzeru ndiye mwamuna wamphamvu,+ ndipo munthu wodziwa zinthu amachulukitsa mphamvu zake.+ Mlaliki 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ineyo ndinati: “Nzeru n’zabwino kuposa mphamvu,+ koma nzeru za munthu wosauka zimanyozedwa ndipo anthu samvera mawu ake.”+
16 Ndiyeno mkazi wina wanzeru+ mumzindawo anayamba kufuula kuti: “Tamverani amuna inu, tamverani! Chonde muuzeni Yowabu kuti abwere pafupipa kuti ndilankhule naye.”
5 Munthu amene amagwiritsa ntchito mphamvu zake mwanzeru ndiye mwamuna wamphamvu,+ ndipo munthu wodziwa zinthu amachulukitsa mphamvu zake.+
16 Choncho ineyo ndinati: “Nzeru n’zabwino kuposa mphamvu,+ koma nzeru za munthu wosauka zimanyozedwa ndipo anthu samvera mawu ake.”+