Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 10:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma zili ngati mudzi wake wolimba.+ Chiwonongeko cha onyozeka ndicho umphawi wawo.+

  • Maliko 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kodi iyeyu si mmisiri wamatabwa,+ mwana wa Mariya,+ komanso m’bale wake wa Yakobo,+ Yosefe, Yudasi ndi Simoni?+ Ndipo alongo ake si awa omwe tili nawo pompano?” Choncho anayamba kukhumudwa naye.+

  • Yohane 7:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Palibe ndi mmodzi yemwe mwa olamulira kapena Afarisi amene wakhulupirira mwa iye, alipo ngati?+

  • 1 Akorinto 1:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma Mulungu anasankha zopusa za dziko+ kuti achititse manyazi anthu anzeru, ndipo Mulungu anasankha zinthu zofooka za dziko kuti achititse manyazi+ zinthu zamphamvu.

  • 1 Akorinto 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Palibe wolamulira+ ndi mmodzi yemwe wa nthawi* ino amene anadziwa+ nzeru imeneyi, chifukwa ngati anali kuidziwa sakanapachika+ Ambuye waulemereroyo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena